Yohane 13:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo Yesu anayankha, Ndi iyeyu, amene Ine ndidzamsunsira nthongo ndi kumpatsa. Pamenepo, m'mene anasunsa nthongo anaitenga naipatsa Yudasi mwana wa Simoni Iskariote. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo Yesu anayankha, Ndi iyeyu, amene Ine ndidzamsunsira nthongo ndi kumpatsa. Pamenepo, m'mene anasunsa nthongo anaitenga naipatsa Yudasi mwana wa Simoni Iskariote. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Yesu adati, “Yemwe ndimusunsire nkumupatsa mkate umene ndimunyemere ndi ameneyo.” Tsono atasunsa mkate wonyemawo adaupatsa Yudasi, mwana wa Simoni Iskariote. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Yesu anayankha kuti, “Iye amene ndidzamupatsa buledi amene ndanyema ndikususa ndi ameneyo.” Kenaka, atasunsa gawo la buledi, Iye anapereka kwa Yudasi Isikarioti, mwana wa Simoni. Onani mutuwo |