Yohane 13:25 - Buku Lopatulika25 Iyeyu potsamira pomwepo, pa chifukwa cha Yesu, anena ndi Iye, Ambuye, ndiye yani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Iyeyu potsamira pomwepo, pa chifukwa cha Yesu, anena ndi Iye, Ambuye, ndiye yani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pamenepo iyeyo adatsamira pachifukwa pa Yesu, namufunsa kuti, “Ambuye, mukunena yani kodi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Atamutsamiranso Yesuyo, anamufunsa Iye kuti, “Ambuye, kodi ndani?” Onani mutuwo |