Yohane 13:21 - Buku Lopatulika21 Yesu m'mene adanena izi, anavutika mumzimu, nachita umboni, nati, Indetu, indetu, ndinena ndi inu, kuti mmodzi wa inu adzandipereka Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Yesu m'mene adanena izi, anavutika mumzimu, nachita umboni, nati, Indetu, indetu, ndinena ndi inu, kuti mmodzi wa inu adzandipereka Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Yesu atanena zimenezi, adayamba kuvutika mu mtima ndipo adati, “Ndinene poyera pano: mmodzi mwa inu andipereka kwa adani anga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Yesu atanena izi, anavutika kwambiri mu mzimu ndipo anachitira umboni kuti, “Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti mmodzi mwa inu adzandipereka.” Onani mutuwo |