Yohane 13:20 - Buku Lopatulika20 Indetu, indetu, ndinena ndi inu, Iye wolandira aliyense amene ndimtuma, andilandira Ine; koma wolandira Ine alandira wondituma Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Indetu, indetu, ndinena ndi inu, Iye wolandira amene aliyense ndimtuma, andilandira Ine; koma wolandira Ine alandira wondituma Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ndithu ndikunenetsa kuti wolandira aliyense amene ndamtuma, amalandira Ine. Ndipo wondilandira Ine, amalandira Iye amene adandituma.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti aliyense amene alandira amene Ine ndamutuma, alandiranso Ine. Aliyense amene alandira Ine, alandiranso amene anandituma.” Onani mutuwo |