Yohane 13:16 - Buku Lopatulika16 Indetu, indetu, ndinena ndi inu, Kapolo sali wamkulu ndi mbuye wake; kapena mtumwi sali wamkulu ndi womtuma iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Indetu, indetu, ndinena ndi inu, Kapolo sali wamkulu ndi mbuye wake; kapena mtumwi sali wamkulu ndi womtuma iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Kunena zoona, wantchito saposa mbuye wake, nthumwinso siiposa woituma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti wantchito saposa mbuye wake, kapena wotumidwa kuposa amene wamutuma. Onani mutuwo |