Yohane 12:44 - Buku Lopatulika44 Koma Yesu anafuula nati, Iye wokhulupirira Ine, sakhulupirira Ine, koma Iye wondituma Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Koma Yesu anafuula nati, Iye wokhulupirira Ine, sakhulupirira Ine, koma Iye wondituma Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Yesu adanena mokweza mau kuti, “Munthu wondikhulupirira, sakhulupirira Ine ndekha ai, koma amakhulupiriranso Iye amene adandituma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Kenaka Yesu anafuwula nati, “Munthu aliyense amene akhulupirira Ine, sakhulupirira Ine ndekha, komanso Iye amene anandituma Ine. Onani mutuwo |