Yohane 12:43 - Buku Lopatulika43 pakuti anakonda ulemerero wa anthu koposa ulemerero wa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 pakuti anakonda ulemerero wa anthu koposa ulemerero wa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Ankakonda kuti azilandira ulemu kwa anthu koposa kulandira ulemu kwa Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 pakuti iwo amakonda kuyamikiridwa ndi anthu kuposa kuyamikiridwa ndi Mulungu. Onani mutuwo |