Yohane 12:41 - Buku Lopatulika41 Izi anati Yesaya, chifukwa anaona ulemerero wake; nalankhula za Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Izi anati Yesaya, chifukwa anaona ulemerero wake; nalankhula za Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Yesaya ponena mau amenewo, ankanena za Yesu, chifukwa adaaona ulemerero wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Yesaya ananena izi chifukwa anaona ulemerero wa Yesu ndi kuyankhula za Iye. Onani mutuwo |