Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 12:30 - Buku Lopatulika

30 Yesu anayankha nati, Mau awa sanafike chifukwa cha Ine, koma cha inu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Yesu anayankha nati, Mau awa sanafika chifukwa cha Ine, koma cha inu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Yesu adaŵauza kuti, “Mauŵa amveka osati chifukwa cha Ine ai, koma chifukwa cha inu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Yesu anati, “Mawu awa abwera chifukwa cha inu osati chifukwa cha Ine.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 12:30
5 Mawu Ofanana  

Ndipo ndikondwera chifukwa cha inu kuti kunalibe Ine komweko, chakuti mukakhulupirire; koma tiyeni, tipite kwa iye.


Koma ndadziwa Ine kuti mumandimva Ine nthawi zonse; koma chifukwa cha khamu la anthu alikuimirira pozungulira ndinanena ichi, kuti akhulupirire kuti Inu munandituma Ine.


Tsopano pali kuweruza kwa dziko ili lapansi; mkulu wa dziko ili lapansi adzatayidwa kunja tsopano.


Ndipo Ine sindilandira umboni kwa munthu: koma ndinena izi, kuti inu mukapulumutsidwe.


Pakuti mudziwa chisomo cha Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti, chifukwa cha inu anakhala wosauka, angakhale anali wolemera, kuti inu ndi kusauka kwake mukakhale olemera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa