Yohane 12:22 - Buku Lopatulika22 Filipo anadza nanena kwa Andrea; nadza Andrea ndi Filipo, nanena ndi Yesu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Filipo anadza nanena kwa Andrea; nadza Andrea ndi Filipo, nanena ndi Yesu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Filipo adakauza Andrea, ndipo Andrea pamodzi ndi Filipoyo adakauza Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Filipo anapita kukawuza Andreya; Andreya ndi Filipo pamodzi anakawuza Yesu. Onani mutuwo |