Yohane 12:23 - Buku Lopatulika23 Koma Yesu anayankha iwo, nati, Yafika nthawi, kuti Mwana wa Munthu alemekezedwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Koma Yesu anayankha iwo, nati, Yafika nthawi, kuti Mwana wa Munthu alemekezedwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Yesu adati, “Yafika nthaŵi yoti Mwana wa Munthu alandire ulemerero wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Yesu anayankha kuti, “Nthawi yafika yakuti Mwana wa Munthu alemekezedwe. Onani mutuwo |