Yohane 11:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo pambuyo pake ananena kwa ophunzira ake, Tiyeni tipitenso ku Yudeya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo pambuyo pake ananena kwa ophunzira ake, Tiyeni tipitenso ku Yudeya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pambuyo pake adauza ophunzira ake kuti, “Tiyeni tipitenso ku Yudeya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kenaka anati kwa ophunzira ake, “Tiyeni tibwerere ku Yudeya.” Onani mutuwo |