Yohane 11:8 - Buku Lopatulika8 Ophunzira ananena ndi Iye, Rabi, Ayuda analikufuna kukuponyani miyala tsopano apa; ndipo munkanso komweko kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ophunzira ananena ndi Iye, Rabi, Ayuda analikufuna kukuponyani miyala tsopano apa; ndipo munkanso komweko kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ophunzira akewo adati, “Aphunzitsi, tsopano apa Ayuda ankafuna kukuponyani miyala, ndiye mukuti mupitenso komweko?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ophunzira akewo anati, “Rabi, posachedwa pomwepa Ayuda anafuna kukugendani ndi miyala, koma Inu mukupitanso komweko?” Onani mutuwo |