Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 11:6 - Buku Lopatulika

6 Chifukwa chake pamene anamva kuti anadwala, anakhala pamenepo pamalo pomwepo masiku awiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Chifukwa chake pamene anamva kuti anadwala, anakhala pamenepo pa malo pomwepo masiku awiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Komabe pamene adamva za matendawo, Yesu adaswera masiku aŵiri pamalo pomwe adaaliripo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Koma atamva kuti Lazaro akudwala, Iye anakhalabe kumene anali masiku ena awiri.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 11:6
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Abrahamu anatcha dzina lake la malowo Yehova-Yire: monga ati lero lomwe, M'phiri la Yehova chidzaoneka.


Ndipo anawafotokozera iwo nalira, nawatembenukiranso, nanena nao, nampatula Simeoni mwa iwo, nammanga iye pamaso pao.


Chifukwa chake Yehova adzadikira, kuti akukomereni mtima, ndipo chifukwa chake Iye adzakuzidwa, kuti akuchitireni inu chifundo; pakuti Yehova ndiye Mulungu wa chiweruziro; odala ali onse amene amdikira Iye.


Koma Yesu anakonda Marita, ndi mbale wake, ndi Lazaro.


Ndipo pambuyo pake ananena kwa ophunzira ake, Tiyeni tipitenso ku Yudeya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa