Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 11:57 - Buku Lopatulika

57 Koma ansembe aakulu ndi Afarisi adalamula kuti, munthu wina akadziwa pokhala Iye, aulule, kuti akamgwire Iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

57 Koma ansembe aakulu ndi Afarisi adalamula kuti, munthu wina akadziwa pokhala Iye, aulule, kuti akamgwire Iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

57 Koma akulu a ansembe ndi Afarisi anali atalamula kuti aliyense akadziŵa kumene kuli Yesu, aŵadziŵitse, kuti akamgwire.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

57 Koma akulu a ansembe ndi Afarisi anapereka lamulo kuti ngati wina aliyense adziwe kumene kunali Yesu, iye akawawuze kuti akamugwire.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 11:57
7 Mawu Ofanana  

M'malo mwa chikondi changa andibwezera udani; koma ine, kupemphera ndiko.


Anafunanso kumgwira Iye; ndipo anapulumuka m'dzanja lao.


Koma ena a mwa iwo anamuka kwa Afarisi, nawauza zimene Yesu adazichita.


Pamenepo ansembe aakulu ndi Afarisi anasonkhanitsa akulu, nanena, Titani ife? Chifukwa munthu uyu achita zizindikiro zambiri.


Pamenepo anatola miyala kuti amponye Iye; koma Yesu anabisala, natuluka mu Kachisi.


Izi ananena atate wake ndi amake, chifukwa anaopa Ayuda; pakuti Ayuda adapangana kale, kuti ngati munthu aliyense adzamvomereza Iye kuti ndiye Khristu, akhale woletsedwa m'sunagoge.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa