Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 11:56 - Buku Lopatulika

56 Pamenepo analikumfuna Yesu, nanena wina ndi mnzake poimirira iwo mu Kachisi, Muyesa bwanji inu, sadzadza kuchikondwerero kodi?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

56 Pamenepo analikumfuna Yesu, nanena wina ndi mnzake poimirira iwo m'Kachisi, Muyesa bwanji inu, sadzadza kuchikondwerero kodi?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

56 Ankamufunafuna Yesu, ndipo pamene adasonkhana m'Nyumba ya Mulungu ankafunsana kuti, “Kodi inu mukuganiza bwanji? Kodi monga Iye uja abwera kuchikondwerero kuno?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

56 Iwo anapitiriza kumufunafuna Yesu, ndipo pamene ankayimirira mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu anafunsana wina ndi mnzake kuti, “Kodi ukuganiza chiyani? Kodi Iye sabwera konse kuphwando?”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 11:56
3 Mawu Ofanana  

Koma ansembe aakulu ndi Afarisi adalamula kuti, munthu wina akadziwa pokhala Iye, aulule, kuti akamgwire Iye.


Pomwepo Ayuda analikumfuna Iye pachikondwerero, nanena, Ali kuti uja?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa