Yohane 11:29 - Buku Lopatulika29 Koma iyeyo, pakumva, ananyamuka msanga, nadza kwa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Koma iyeyo, pakumva, ananyamuka msanga, nadza kwa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Maria atamva zimenezi, adanyamuka msangamsanga, nadza kwa Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Mariya atamva izi, anayimirira mofulumira napita kwa Iye. Onani mutuwo |