Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 11:30 - Buku Lopatulika

30 (Koma Yesu sanafike kumudzi, koma anali pamalo pomwe Marita adakomana ndi Iye.)

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 (Koma Yesu sanafike kumudzi, koma anali pamalo pomwe Marita adakomana ndi Iye.)

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Pamenepo nkuti Yesu asanafike kumudziko, koma anali chikhalire pamalo pomwe Marita adaakumana naye.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Tsopano nʼkuti Yesu asanalowe mʼmudzi, koma anali akanali pa malo pamene Marita anakumana naye.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 11:30
3 Mawu Ofanana  

Pamenepo Marita, pakumva kuti Yesu alinkudza, anamuka kukakomana ndi Iye; koma Maria anakhalabe m'nyumba.


Ndipo m'mene anati ichi anachoka naitana Maria mbale wake m'tseri, ndi kuti, Wafika Mphunzitsi, akuitana iwe.


Koma iyeyo, pakumva, ananyamuka msanga, nadza kwa Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa