Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 11:20 - Buku Lopatulika

20 Pamenepo Marita, pakumva kuti Yesu alinkudza, anamuka kukakomana ndi Iye; koma Maria anakhalabe m'nyumba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Pamenepo Marita, pakumva kuti Yesu alinkudza, anamuka kukakomana ndi Iye; koma Maria anakhalabe m'nyumba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Pamene Marita adamva kuti Yesu akubwera, adapita kukamchingamira. Koma Maria adaatsalira m'nyumba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Pamene Marita anamva kuti Yesu akubwera, anapita kukakumana naye. Koma Mariya anatsala ku nyumba.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 11:20
7 Mawu Ofanana  

Pomwepo Ufumu wa Kumwamba udzafanizidwa ndi anamwali khumi, amene anatenga nyali zao, natuluka kukakomana ndi mkwati.


Koma pakati pa usiku panali kufuula, Onani, mkwati! Tulukani kukakomana naye.


(Koma Yesu sanafike kumudzi, koma anali pamalo pomwe Marita adakomana ndi Iye.)


Ndipo panali pakulowa Petro, Kornelio anakomana naye, nagwa pa mapazi ake, namlambira.


Kuchokera kumeneko abalewo, pakumva za ife, anadza kukomana nafe ku Bwalo la Apio, ndi ku Nyumba za Alendo Zitatu; ndipo pamene Paulo anawaona, anayamika Mulungu, nalimbika mtima.


pamenepo ife okhala ndi moyo, otsalafe, tidzakwatulidwa nao pamodzi m'mitambo, kukakomana ndi Ambuye mumlengalenga, ndipo potero tidzakhala ndi Ambuye nthawi zonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa