Yohane 11:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo pamene Yesu anadza, anapeza kuti pamenepo atakhala m'manda masiku anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo pamene Yesu anadza, anapeza kuti pamenepo atakhala m'manda masiku anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Pamene Yesu adafika ku Betaniya, adapeza Lazaro atagona m'manda masiku anai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Yesu atafika, anapeza kuti Lazaro anali atagona mʼmanda masiku anayi. Onani mutuwo |