Yohane 11:13 - Buku Lopatulika13 Koma Yesu adanena za imfa yake; koma iwowa anayesa kuti ananena za mpumulo wa tulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma Yesu adanena za imfa yake; koma iwowa anayesa kuti ananena za mpumulo wa tulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Iwo ankayesa kuti akunena za tulo teniteni, koma Yesu ankanena za imfa yake ya Lazaro. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Yesu ankayankhula za imfa yake koma ophunzira ake ankaganiza kuti amanena za tulo chabe. Onani mutuwo |