Yohane 11:12 - Buku Lopatulika12 Chifukwa chake ophunzira ake anati kwa Iye, Ambuye, ngati ali m'tulo adzachira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Chifukwa chake ophunzira ake anati kwa Iye, Ambuye, ngati ali m'tulo adzachira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Apo ophunzira ake adati, “Ambuye, ngati wagona tulo, achira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ophunzira ake anayankha kuti, “Ambuye, ngati wagona adzapeza bwino.” Onani mutuwo |