Yohane 10:8 - Buku Lopatulika8 Onse amene anadza m'tsogolo mwa Ine ali akuba, ndi olanda: koma nkhosa sizinamve iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Onse amene anadza m'tsogolo mwa Ine ali akuba, ndi olanda: koma nkhosa sizinamva iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ena onse amene adabwera Ine ndisanafike, ngakuba ndi olanda, koma nkhosa sizinaŵamvere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Onse amene anadza ndisanabwere Ine ndi akuba ndi achifwamba, ndipo nkhosa sizinawamvere. Onani mutuwo |