Yohane 10:9 - Buku Lopatulika9 Ine ndine khomo; ngati wina alowa ndi Ine, adzapulumutsidwa, nadzalowa, nadzatuluka, nadzapeza busa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ine ndine khomo; ngati wina alowa ndi Ine, adzapulumutsidwa, nadzalowa, nadzatuluka, nadzapeza busa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Khomo ndine. Munthu akaloŵera pa Ine, adzapulumuka. Azidzaloŵa ndi kutuluka, ndipo adzapeza chakudya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ine ndine khomo, aliyense amene alowa kudzera mwa Ine adzapulumuka. Iye adzalowa ndi kutuluka ndi kupeza msipu. Onani mutuwo |