Yohane 10:6 - Buku Lopatulika6 Fanizo ili Yesu ananena kwa iwo; koma sanazindikire zimene Yesu analikulankhula nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Fanizo ili Yesu ananena kwa iwo; koma sanazindikira zimene Yesu analikulankhula nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Yesu adaŵaphera fanizoli, koma iwo sadamvetse zimene ankaŵauzazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Yesu ananena mawu ophiphiritsawa, koma Afarisi sanazindikire zimene ankawawuza. Onani mutuwo |