Yohane 10:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo Yesu analikuyendayenda mu Kachisi m'khonde la Solomoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo Yesu analikuyendayenda m'Kachisi m'khonde la Solomoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Yesu ankangodziyendera m'Nyumba ya Mulungu, m'khonde lotchedwa Khonde la Solomoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 ndipo Yesu ankayenda mʼbwalo la Nyumbayo ku malo a Solomoni. Onani mutuwo |