Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 10:22 - Buku Lopatulika

22 Koma kunali phwando la kukonzetsanso mu Yerusalemu; nyengoyo ndi yachisanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Koma kunali phwando la kukonzetsanso m'Yerusalemu; nyengoyo ndi yachisanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Ku Yerusalemu kunali chikondwerero chokumbukira kuperekedwanso kwa Nyumba ya Mulungu. Inali nyengo yozizira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Ku Yerusalemu kunali chikondwerero chokumbukira kupatulidwa kwa Nyumba ya Mulungu. Inali nthawi yozizira,

Onani mutuwo Koperani




Yohane 10:22
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Solomoni anaphera nsembe yamtendere, yophera kwa Yehova ng'ombe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, ndi nkhosa zikwi zana limodzi mphambu makumi awiri. Momwemo mfumu ndi ana a Israele onse anapereka nyumbayo ya Yehova.


Ndipo mfumu Solomoni anapereka nsembe ya ng'ombe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, ndi nkhosa zikwi makumi awiri. Momwemo mfumu ndi anthu onse anapereka nyumba ya Mulungu.


Ndipo ana a Israele, ansembe ndi Alevi, ndi ana otsala a ndende, anapereka nyumba iyi ya Mulungu mokondwera.


Ndipo alembi amene adatsika ku Yerusalemu ananena kuti, Ali naye Belezebulu, ndipo, Ndi mkulu wao wa ziwanda atulutsa ziwanda.


Ena ananena, Mau awa sali a munthu wogwidwa chiwanda. Kodi chiwanda chikhoza kumtsegulira maso wosaona?


Ndipo Yesu analikuyendayenda mu Kachisi m'khonde la Solomoni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa