Yohane 10:21 - Buku Lopatulika21 Ena ananena, Mau awa sali a munthu wogwidwa chiwanda. Kodi chiwanda chikhoza kumtsegulira maso wosaona? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ena ananena, Mau awa sali a munthu wogwidwa chiwanda. Kodi chiwanda chikhoza kumtsegulira maso wosaona? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma ena ankati, “Mau ameneŵa si a munthu wogwidwa ndi mizimu yoipa. Kodi mizimu yoipa nkupenyetsa anthu akhungu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma ena anati, “Awa si mawu a munthu wogwidwa ndi ziwanda. Kodi ziwanda zingathe bwanji kutsekula maso a wosaona?” Onani mutuwo |