Yohane 10:13 - Buku Lopatulika13 chifukwa ali wolipidwa, ndipo sasamala nkhosa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 chifukwa ali wolipidwa, ndipo sasamala nkhosa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Wolembedwa ntchito uja amathaŵa, chifukwa amangotsata malipiro chabe, ndipo salabadirako za nkhosazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Munthuyo amathawa chifukwa ndi wantchito ndipo sasamalira chilichonse cha nkhosazo. Onani mutuwo |