Yohane 10:14 - Buku Lopatulika14 Ine ndiye Mbusa Wabwino; ndipo ndizindikira zanga, ndi zanga zindizindikira Ine, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ine ndiye Mbusa Wabwino; ndipo ndizindikira zanga, ndi zanga zindizindikira Ine, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Mbusa wabwino ndine. Nkhosa zanga ndimazidziŵa, ndipo izozo Ineyo zimandidziŵa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 “Ine ndine mʼbusa wabwino. Ine ndimazidziwa nkhosa zanga ndipo nkhosa zangazo zimandidziwa, Onani mutuwo |