Yohane 1:9 - Buku Lopatulika9 Uku ndiko kuunika kwenikweni, kumene kuunikira anthu onse akulowa m'dziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Uku ndiko kuunika kwenikweni, kumene kuunikira anthu onse akulowa m'dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kuŵala kwenikweni, kounikira anthu onse, kunkadza pansi pano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kuwunika koona kumene kuwunikira munthu aliyense kunabwera ku dziko lapansi. Onani mutuwo |