Yohane 1:10 - Buku Lopatulika10 Anali m'dziko lapansi, ndi dziko linalengedwa ndi Iye, koma dziko silinamzindikira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Anali m'dziko lapansi, ndi dziko linalengedwa ndi Iye, koma dziko silinamzindikira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Wotchedwa Mauyo anali m'dziko lapansi, ndipo Mulungu adalenga dziko lapansilo kudzera mwa Iye, komabe anthu apansipano sadamzindikire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iye anali mʼdziko lapansi, ndipo ngakhale kuti dziko lapansi linalengedwa ndi Iye, dziko lapansilo silinamuzindikire Iye. Onani mutuwo |