Yohane 1:8 - Buku Lopatulika8 Iye sindiye kuunikaku, koma anatumidwa kukachita umboni wa kuunikaku. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Iye sindiye kuunikaku, koma anatumidwa kukachita umboni wa kuunikaku. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Sikuti iyeyo ndiye anali kuŵalako ai, koma adangobwera kudzachitira umboni kuŵalako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iyeyu sanali kuwunika; koma anabwera ngati mboni ya kuwunika. Onani mutuwo |