Yohane 1:7 - Buku Lopatulika7 Iyeyu anadza mwa umboni kudzachita umboni za kuunikaku, kuti onse akakhulupirire mwa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Iyeyu anadza mwa umboni kudzachita umboni za kuunikaku, kuti onse akakhulupirire mwa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Iyeyu adaabwera ngati mboni, kudzachitira umboni kuŵala kuja, kuti anthu onse akhulupirire chifukwa cha umboni wakewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye anabwera ngati mboni kudzachitira umboni kuwunikako kuti kudzera mwa iye anthu onse akhulupirire. Onani mutuwo |