Yohane 1:6 - Buku Lopatulika6 Kunali munthu, wotumidwa ndi Mulungu, dzina lake ndiye Yohane. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kunali munthu, wotumidwa ndi Mulungu, dzina lake ndiye Yohane. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mulungu adaatuma munthu wina, dzina lake Yohane. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kunabwera munthu amene anatumizidwa kuchokera kwa Mulungu; Iyeyo dzina lake linali Yohane. Onani mutuwo |