Yohane 1:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo kuunikaku kunawala mumdima; ndi mdimawu sunakuzindikire. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo kuunikaku kunawala mumdima; ndi mdimawu sunakuzindikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Kuŵalako kukuunikabe mu mdima, ndipo mdima sudathe kugonjetsa kuŵalako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Kuwunika kunawala mu mdima, koma mdimawo sunakuzindikire. Onani mutuwo |