Yohane 1:46 - Buku Lopatulika46 Natanaele anati kwa iye, Ku Nazarete nkutha kuchokera kanthu kabwino kodi? Filipo ananena naye, Tiye ukaone. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201446 Natanaele anati kwa iye, Ku Nazarete nkutha kuchokera kanthu kabwino kodi? Filipo ananena naye, Tiye ukaone. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa46 Koma Natanaele adamufunsa kuti, “Kodi ku Nazarete nkuchokera kanthu kabwino?” Filipo adati, “Tiye ukadziwonere wekha.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero46 Natanieli anafunsa kuti, “Nazareti! Kodi kanthu kalikonse kabwino kangachokere kumeneko?” Filipo anati, “Bwera udzaone.” Onani mutuwo |