Yohane 1:41 - Buku Lopatulika41 Anayamba iye kupeza mbale wake yekha Simoni, nanena naye, Tapeza ife Mesiya (ndiko kusandulika Khristu). Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Anayamba iye kupeza mbale wake yekha Simoni, nanena naye, Tapeza ife Mesiya (ndiko kusandulika Khristu). Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Iye adayamba kukapeza mbale wakeyo Simoni, namuuza kuti, “Tampeza Mesiya.” (Ndiye kuti, Mpulumutsi wolonjezedwa uja.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Choncho chimene Andreya anachita ndi kukapeza mʼbale wake Simoni ndipo anamuwuza kuti, “Ife tamupeza Mesiya,” (kutanthauza kuti Khristu). Onani mutuwo |