Yohane 1:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo ndaona ine, ndipo ndachita umboni kuti Mwana wa Mulungu ndi Yemweyu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo ndaona ine, ndipo ndachita umboni kuti Mwana wa Mulungu ndi Yemweyu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Ineyo ndidaziwonadi, ndipo ndikuchita umboni kuti ameneyu ndi Mwanadi wa Mulungu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Ine ndaona ndipo ndikuchitira umboni kuti uyu ndi Mwana wa Mulungu.” Onani mutuwo |