Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 1:35 - Buku Lopatulika

35 M'mawa mwakenso analikuimirira Yohane ndi awiri a ophunzira ake;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

35 M'mawa mwakenso analikuimirira Yohane ndi awiri a ophunzira ake;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

35 M'maŵa mwakenso Yohane anali pamalo pomwepo pamodzi ndi ophunzira ake ena aŵiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

35 Pa tsiku lotsatira Yohane analinso pamenepo pamodzi ndi awiri a ophunzira ake.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 1:35
5 Mawu Ofanana  

Pamenepo iwo akuopa Yehova analankhulana wina ndi mnzake; ndipo Yehova anawatchera khutu namva, ndi buku la chikumbutso linalembedwa pamaso pake, la kwa iwo akuopa Yehova, nakumbukira dzina lake.


M'mawa mwake anaona Yesu alinkudza kwa iye, nanena, Onani Mwanawankhosa wa Mulungu amene achotsa tchimo lake la dziko lapansi!


M'mawa mwake anafuna kutuluka kunka ku Galileya, napeza Filipo. Ndipo Yesu ananena naye, Tsata Ine.


Ndipo tsiku lachitatu panali ukwati mu Kana wa mu Galileya; ndipo amake wa Yesu anali komweko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa