Yeremiya 9:1 - Buku Lopatulika1 Ha, mutu wanga ukadakhala madzi, ndi maso anga kasupe wa misozi, kuti usana ndi usiku ndilirire ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ha, mutu wanga ukadakhala madzi, ndi maso anga kasupe wa misozi, kuti usana ndi usiku ndilirire ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ndikadakonda kuti mutu wanga ukhale ngati chitsime cha madzi, kuti maso anga akhale ngati kasupe wa misozi, kuti ndilire usana ndi usiku, kulirira onse amene adafa a mtundu wa anthu anga? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Aa, ndikanakonda kuti mutu wanga ukanakhala chitsime cha madzi, ndi maso anga ngati kasupe wa misozi! Ndikanalira usana ndi usiku kulirira anthu anga amene aphedwa. Onani mutuwo |