Yeremiya 8:8 - Buku Lopatulika8 Bwanji muti, Tili ndi nzeru ife, ndi malamulo a Yehova ali ndi ife? Koma, taona, peni lonyenga la alembi lachita zonyenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Bwanji muti, Tili ndi nzeru ife, ndi malamulo a Yehova ali ndi ife? Koma, taona, peni lonyenga la alembi lachita zonyenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 “Mungathe kunena bwanji kuti, ‘Ndife anzeru, timasunga malamulo a Chauta, pamene alembi akulemba zabodza?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “ ‘Inu mukunena bwanji kuti, ‘Ndife anzeru ndipo timasunga malamulo a Yehova?’ Koma ndi alembi anu amene akulemba zabodza. Onani mutuwo |