Yeremiya 8:7 - Buku Lopatulika7 Inde, chumba cha mlengalenga chidziwa nyengo zake; ndipo njiwa ndi namzeze ndi chingalu ziyang'anira nyengo yakufika kwao; koma anthu anga sadziwa chiweruziro cha Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Inde, chumba cha mlengalenga chidziwa nyengo zake; ndipo njiwa ndi namzeze ndi chingalu ziyang'anira nyengo yakufika kwao; koma anthu anga sadziwa chiweruziro cha Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mbalame amati kapande ija imadziŵa nthaŵi yake mumlengalenga. Nkhunda, namzeze ndi ngalu zimadziŵa nthaŵi yake yonyamukira ulendo. Koma anthu anga sadziŵa malangizo a Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mbalame yotchedwa kakowa ija imadziwa nthawi yake mlengalenga. Koma nkhunda, namzeze ndi chingalu zimadziwa nthawi yonyamukira ulendo, koma anthu anga sadziwa malamulo a Yehova. Onani mutuwo |