Yeremiya 6:9 - Buku Lopatulika9 Yehova wa makamu atero, Adzakunkha otsalira a Israele monga mpesa; bweza dzanja lako monga wakutchera mphesa m'madengu ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Yehova wa makamu atero, Adzakunkha otsalira a Israele monga mpesa; bweza dzanja lako monga wakutchera mphesa m'madengu ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mau a Chauta Wamphamvuzonse akuti, “Akunkheni ndi kuŵalanda zonse anthu otsala a Aisraele, monga momwe anthu amachitira, populula mphesa ku nthambi zake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yehova Wamphamvuzonse anandiwuza kuti, “Adani adzawakunkha ndithu anthu otsala a Israeli, monga momwe amachitira populula mphesa. Tsono iwe yesetsa kupulumutsa amene ungathe monga mmene amachitira munthu wokolola mphesa.” Onani mutuwo |