Yeremiya 52:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo iye anachita zoipa pamaso pa Yehova, monga mwa zonse anazichita Yehoyakimu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo iye anachita zoipa pamaso pa Yehova, monga mwa zonse anazichita Yehoyakimu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Zedekiyayo adachita zoipa pamaso pa Chauta potsata zonse zimene ankachita Yehoyakimu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anachita zoyipa pamaso pa Yehova, monga momwe anachitira Yehoyakimu. Onani mutuwo |