Yeremiya 48:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti adzakwera pa chikweza cha Luhiti ndi kulira kosaleka; pakuti pa chitsiko cha Horonaimu amva kulira kowawa kwa chionongeko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti adzakwera pa chikweza cha Luhiti ndi kulira kosaleka; pakuti pa chitsiko cha Horonaimu amva kulira kowawa kwa chionongeko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Anthu akupita nalira kwambiri pa chikwera cha ku Luhiti. Kulira kwa chiwonongeko kukumveka ku matsitso a ku Horonaimu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Anthu akukwera chikweza cha ku Luhiti, akulira kwambiri pamene akupita. Kulira chifukwa cha chiwonongeko kukumveka pa njira yotsikira ku Horonaimu. Onani mutuwo |