Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yeremiya 48:4 - Buku Lopatulika

4 Mowabu waonongedwa; ang'ono ake amveketsa kulira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Mowabu waonongedwa; ang'ono ake amveketsa kulira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Mowabu waonongeka, ana ake akulira kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Mowabu wawonongeka; ana ake angʼonoangʼono akulira kwambiri.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 48:4
6 Mawu Ofanana  

m'menemo mfumu inalola Ayuda okhala mu mzinda uliwonse asonkhane, ndi kulimbikira moyo wao, kuononga, kupha, ndi kupulula mphamvu yonse ya anthu ndi ya dziko yofuna kuwathira nkhondo, iwo, ana ao aang'ono, ndi akazi ao, ndi kulanda zofunkha zao,


Wodala iye amene adzagwira makanda ako, ndi kuwaphwanya pathanthwe.


Munthuyo akhale ngati mizinda imene Yehova anapasula, osalekerera; amve mfuu mamawa, ndi mkuwo pausana;


Mau amveka kuchokera ku Horonaimu, kufunkha ndi kuononga kwakukulu!


Pakuti adzakwera pa chikweza cha Luhiti ndi kulira kosaleka; pakuti pa chitsiko cha Horonaimu amva kulira kowawa kwa chionongeko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa