Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yeremiya 48:6 - Buku Lopatulika

6 Thawani, pulumutsani miyoyo yanu, mukhale amaliseche m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Thawani, pulumutsani miyoyo yanu, mukhale amaliseche m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Thaŵani, mudzipulumutse. Thamangani ngati mbidzi yam'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Thawani! Dzipulumutseni; khalani ngati mbidzi ya mʼchipululu.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 48:6
10 Mawu Ofanana  

Ndipo panali pamene anawatulutsa iwo kunja, anati, Tapulumuka ndi moyo wako; usacheuke, usakhale pachigwa paliponse; thawira kuphiri, kuti unganyeke.


Ndakhulupirira Yehova, mutani nkunena kwa moyo wanga, Thawirani kuphiri lanu ngati mbalame?


Ndipo adzakhala ngati tsanya la m'chipululu, ndipo saona pamene chifika chabwino; koma adzakhala m'malo oumitsa m'chipululu, dziko lachikungu lopanda anthu.


Thawani pakati pa Babiloni, yense apulumuke moyo wake; musathedwe m'choipa chake; pakuti ndi nthawi ya kubwezera chilango; Yehova adzambwezera iye mphotho yake.


Chifukwa chake iye ananena kwa makamuwo a anthu amene anatulukira kukabatizidwa ndi iye, Obadwa a njoka inu, anakulangizani inu ndani kuthawa mkwiyo ulinkudza?


kuti mwa zinthu ziwiri zosasinthika, m'mene Mulungu sangathe kunama, tikakhale nacho chotichenjeza cholimba, ife amene tidathawira kuchigwira chiyembekezo choikika pamaso pathu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa