Yeremiya 42:3 - Buku Lopatulika3 kuti Yehova Mulungu wanu atisonyeze ife njira imene tiyendemo, ndi chomwe tichite. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 kuti Yehova Mulungu wanu atisonyeze ife njira imene tiyendemo, ndi chomwe tichite. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mupemphere kuti Chauta, Mulungu wanu atiwuze kumene tiyenera kupita ndi zimene tikachite.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mupemphere kuti Yehova Mulungu wanu atiwuze kumene tiyenera kupita ndi chimene tiyenera kuchita.” Onani mutuwo |