Yeremiya 41:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo dzenje moponyamo Ismaele mitembo yonse ya anthu amene anawapha, chifukwa cha Gedaliya, ndilo analipanga mfumu Asa chifukwa cha kuopa Baasa mfumu ya Israele, lomwelo Ismaele mwana wa Netaniya analidzaza ndi ophedwawo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo dzenje moponyamo Ismaele mitembo yonse ya anthu amene anawapha, chifukwa cha Gedaliya, ndilo analipanga mfumu Asa chifukwa cha kuopa Baasa mfumu ya Israele, lomwelo Ismaele mwana wa Netaniya analidzaza ndi ophedwawo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Chitsime chimene Ismaele adatayamo anthu amene adaŵapha aja chinali chitsime chachikulu chija chimene adaakumba ndi mfumu Asa, ataopsedwa ndi Basa mfumu ya ku Israele. Ismaele, mwana wa Netaniya adachidzaza ndi mitembo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Tsono chitsime chimene anaponyamo mitembo ya anthu amene anawaphawo pamodzi ndi mtembo wa Gedaliya chinali chimene mfumu Asa anachikumba poopsedwa ndi Baasa mfumu ya Israeli. Ismaeli mwana wa Netaliya anachidzaza ndi mitembo. Onani mutuwo |